Abale nyimbo iyi imandipangitsa kulilila moyo wanga komanso myoyo ya abale ndi alongo onse mwa ambuye. Tiyeni tilape ndikulandiya ambuye yesu kuti tikalandile chipulumutso ndi kukayimbila limodzi mu ufumu wake. RSA. I miss home and listen to these music God bless you all dearest brothers and sisters.
ndipo mwanena apa zowona. Mulungu atithandize kukhala miyoyo yobweretsa ulemerero ku dzina lake
mkalikisha 3 months ago in playlist mkalikisha's favourites
Abale nyimbo iyi imandipangitsa kulilila moyo wanga komanso myoyo ya abale ndi alongo onse mwa ambuye. Tiyeni tilape ndikulandiya ambuye yesu kuti tikalandile chipulumutso ndi kukayimbila limodzi mu ufumu wake. RSA. I miss home and listen to these music God bless you all dearest brothers and sisters.
stephanomosesmwana 5 months ago
Mulungu akutsogoleleni
Nditso 10 months ago
This tune is so touching......Glory to God. Abale dzikomo kwambili. I feel home as I am listening to this melody. Missing home.
God bless you
Princejayize 1 year ago
Very touching and lovely song! God bless you for this wonderful music
112493ZN 1 year ago
this song,makes me cry
julia1173 1 year ago
this song its so touchng.....
tiya500 2 years ago
very beautiful
susieQ19876 2 years ago
Nice video. Koma I need home!
Titus1980able 2 years ago
ndakusowa kwathu
kamuyango 2 years ago
may u all be bless too. nc usa
koncaar 2 years ago
Ambuye pliz forgive me sindidzabwerezanso. I miss home and my family
salambula 2 years ago
ndikamamvela nyimbo zimenezi ine kuntima myaaa........! kukusowatu kumudzi
kayp1984 2 years ago
koma this song kumudzi kale amalawi tiyeni pajatu kwanu nkwanu mudalaka joka mnthengo, chaka chino wautali basi ndikavine nyimbo imeneyi
elizabethmbale 2 years ago
Nice song!
Can some body translate it for us, plz.
belmunt 2 years ago
amazing
phatlim 2 years ago
God is good all the time,
msangosaint 3 years ago
it realy touched my heart
saba1456 3 years ago
zokoma ndithu i miss home so much
salambula 3 years ago
Im really blessed by this song...it touches my heart,keep it up guys!!
kayp1984 3 years ago