Added: 3 years ago
From: malawiana1
Views: 21,148
Sort by time | Sort by thread (beta)

Link to this comment:

Share to:

All Comments (19)

Sign In or Sign Up now to post a comment!
  • am zambian but this guy's great. i love malawi too. i just wish one i will visit malawi. can some upload paul banda and chapuka's music. i grew up listening to their music in zambia.

  • zakwathu osati zobera ai original pamalawi tayikeni zonse wawa zimatitengera kwathu wawa

  • Pepa pepa zokhoma eeeeh ndipo nane imeneyi ya ndikhuza kwabasi koma nanga nkutani zikachitika chonchi. Mpaka kukumbusa malemu aaaaah zochema eee ameneyo anazimenya yekha. MBEJERE ndiwo dolo kwabasi ndipo I love your music imeneyi ndiye pure malawian music keep it up.

  • koma ndiye,zenizeni zakwathu,osati zobela,keep it up guys

  • koma ndiye,osati zobela.

  • apa nde munamalizatu obwana sitaliyo iliyonse iri m'menemu onyamata otchaya chim'bebe ochewa hahahaha zikamatere bwezi zikoma tiyeni nazo ombenjere!!!!!!!!!!!!.

  • awa ndi original keep it up

    za local osati zobera ai

  • nthawi imeneyo utagulitsa fodya kukanengo tsono mkuima ku sikimu ku bara koma tsono mkumupha gule.

  • Comment removed

  • Nice message and beat. Keep it up.

  • kuvina uku kumandikumbutsa Ajolomo pakotakota Zotex baba simunthu wamasera kuvina.

  • thanks malawiana for the songs and i ask for more. thanks!!!

  • je ne connais pas la langue mais jaime ta chanson merci beaucoup bonjour de haiti

  • ndakutayira kamtengo mbenjere tiye muuze amvetse i miss you keep it up men your a hero

  • lol mavinidwe akewo.

  • ukuimba nyamata.Keep it up!

  • No the guy is great! munthuyu ndi kawawa. He is preserving miyambi etc. I like him so much

  • Ukuyimba bwino ngakhale ikumveka chi Tanzania(from Mr Nice).Try to be original guys!!!!

  • how old is this

Loading...
Alert icon
0 / 00Unsaved Playlist Return to active list
    1. Your queue is empty. Add videos to your queue using this button:
      or sign in to load a different list.
    Loading...Loading...Saving...
    • Clear all videos from this list
    • Learn more